Zekariya 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pa tsiku limenelo, Yehova adzateteza anthu a ku Yerusalemu.+ Munthu amene wapunthwa* pa tsikulo, adzakhala wamphamvu ngati Davide. Nyumba ya Davide idzawatsogolera ngati Mulungu ndiponso ngati mngelo wa Yehova.+ Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:8 Nsanja ya Olonda,12/15/2007, tsa. 25
8 Pa tsiku limenelo, Yehova adzateteza anthu a ku Yerusalemu.+ Munthu amene wapunthwa* pa tsikulo, adzakhala wamphamvu ngati Davide. Nyumba ya Davide idzawatsogolera ngati Mulungu ndiponso ngati mngelo wa Yehova.+