Zekariya 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Banja la nyumba ya Levi+ lizidzalira palokha, ndipo akazi a mʼbanjali azidzalira paokha. Anthu a mʼbanja la Simeyi+ azidzalira paokha, ndipo akazi a mʼbanjali azidzalira paokha.
13 Banja la nyumba ya Levi+ lizidzalira palokha, ndipo akazi a mʼbanjali azidzalira paokha. Anthu a mʼbanja la Simeyi+ azidzalira paokha, ndipo akazi a mʼbanjali azidzalira paokha.