Zekariya 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti, “Pa tsiku limenelo, ndidzafufuta mayina a mafano mʼdziko lonseli+ ndipo sadzakumbukiridwanso. Ndidzachotsamo aneneri+ komanso mzimu wonyansa.
2 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti, “Pa tsiku limenelo, ndidzafufuta mayina a mafano mʼdziko lonseli+ ndipo sadzakumbukiridwanso. Ndidzachotsamo aneneri+ komanso mzimu wonyansa.