Zekariya 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Munthu aliyense akadzayamba kulosera, bambo ake ndi mayi ake amene anamubereka adzamuuza kuti, ‘Iwe ufa ndithu, chifukwa walankhula zonama mʼdzina la Yehova.’ Ndiyeno bambo ndi mayi akewo adzamulasa chifukwa choti akulosera.+ Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:3 Nsanja ya Olonda,12/1/2007, tsa. 116/15/1989, tsa. 31
3 Munthu aliyense akadzayamba kulosera, bambo ake ndi mayi ake amene anamubereka adzamuuza kuti, ‘Iwe ufa ndithu, chifukwa walankhula zonama mʼdzina la Yehova.’ Ndiyeno bambo ndi mayi akewo adzamulasa chifukwa choti akulosera.+