Zekariya 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pa tsikulo, mneneri aliyense azidzachita manyazi ndi masomphenya ake pamene akulosera. Sadzavalanso chovala chapadera chaubweya+ kuti anamize anthu.
4 Pa tsikulo, mneneri aliyense azidzachita manyazi ndi masomphenya ake pamene akulosera. Sadzavalanso chovala chapadera chaubweya+ kuti anamize anthu.