Zekariya 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Iwe lupanga, nyamuka ubaye mʼbusa wanga.+Ubaye munthu yemwe ndi mnzanga,” watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba. “Ipha mʼbusa+ ndipo nkhosa zake zibalalike.+Ine ndidzalanga nkhosa zonyozeka.” Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:7 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Nsanja ya Olonda,8/15/2011, tsa. 13 Tsiku la Yehova, tsa. 55
7 “Iwe lupanga, nyamuka ubaye mʼbusa wanga.+Ubaye munthu yemwe ndi mnzanga,” watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba. “Ipha mʼbusa+ ndipo nkhosa zake zibalalike.+Ine ndidzalanga nkhosa zonyozeka.”