-
Zekariya 14:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Ndidzasonkhanitsa anthu a mitundu yonse kuti amenyane ndi Yerusalemu. Mzindawu udzalandidwa, katundu wamʼnyumba adzatengedwa ndipo akazi adzagwiriridwa. Hafu ya anthu amumzindawu idzatengedwa kupita kudziko lina, koma anthu otsalawo sadzachotsedwa mumzindawu.
-