-
Zekariya 14:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Pa tsiku limenelo mapazi ake adzaponda paphiri la Maolivi+ lomwe lili moyangʼanizana ndi Yerusalemu mbali yakumʼmawa. Phirili lidzagawanika pakati kuyambira kumʼmawa mpaka kumadzulo* ndipo pakati pake padzakhala chigwa chachikulu kwambiri. Hafu ya phirilo idzasunthira kumpoto ndipo hafu inayo idzasunthira kumʼmwera.
-