Zekariya 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pa tsikulo madzi amoyo+ adzatuluka mu Yerusalemu.+ Hafu ya madziwo idzapita kunyanja yakumʼmawa*+ ndipo hafu inayo idzapita kunyanja ya kumadzulo.*+ Zimenezi zidzachitika mʼnyengo yotentha ndiponso mʼnyengo yozizira. Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:8 Nsanja ya Olonda,2/15/2013, tsa. 214/15/2006, tsa. 29
8 Pa tsikulo madzi amoyo+ adzatuluka mu Yerusalemu.+ Hafu ya madziwo idzapita kunyanja yakumʼmawa*+ ndipo hafu inayo idzapita kunyanja ya kumadzulo.*+ Zimenezi zidzachitika mʼnyengo yotentha ndiponso mʼnyengo yozizira.