Zekariya 14:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mliri umene Yehova adzagwetsere anthu onse a mitundu ina amene amamenyana ndi Yerusalemu+ ndi uwu: Munthu aliyense mnofu wake udzawola ali chiimire, maso ake adzawola ali mʼmalo mwake ndiponso lilime lake lidzawola mʼkamwa mwake. Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:12 Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu,12/2017, tsa. 4 Nsanja ya Olonda,2/15/2013, tsa. 207/1/1996, tsa. 22 Tsiku la Yehova, tsa. 32 Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 157-158
12 Mliri umene Yehova adzagwetsere anthu onse a mitundu ina amene amamenyana ndi Yerusalemu+ ndi uwu: Munthu aliyense mnofu wake udzawola ali chiimire, maso ake adzawola ali mʼmalo mwake ndiponso lilime lake lidzawola mʼkamwa mwake.
14:12 Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu,12/2017, tsa. 4 Nsanja ya Olonda,2/15/2013, tsa. 207/1/1996, tsa. 22 Tsiku la Yehova, tsa. 32 Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 157-158