Zekariya 14:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Aliyense wotsala mwa anthu a mitundu yonse obwera kudzamenyana ndi Yerusalemu, chaka chilichonse+ azidzapita kukagwadira* Mfumu, Yehova wa magulu ankhondo akumwamba,+ ndiponso kukachita nawo Zikondwerero za Misasa.+ Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:16 Nsanja ya Olonda,7/1/1996, ptsa. 22-23
16 Aliyense wotsala mwa anthu a mitundu yonse obwera kudzamenyana ndi Yerusalemu, chaka chilichonse+ azidzapita kukagwadira* Mfumu, Yehova wa magulu ankhondo akumwamba,+ ndiponso kukachita nawo Zikondwerero za Misasa.+