Zekariya 14:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pa tsiku limenelo, pamabelu a mahatchi padzalembedwa mawu akuti ‘Chiyero nʼcha Yehova!’+ Ndipo miphika yakukamwa kwakukulu+ yamʼnyumba ya Yehova idzakhala ngati mbale zolowa+ zapaguwa lansembe.
20 Pa tsiku limenelo, pamabelu a mahatchi padzalembedwa mawu akuti ‘Chiyero nʼcha Yehova!’+ Ndipo miphika yakukamwa kwakukulu+ yamʼnyumba ya Yehova idzakhala ngati mbale zolowa+ zapaguwa lansembe.