Malaki 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova wanena kuti: “Ine ndimakukondani anthu inu.”+ Koma inu mwanena kuti: “Mwasonyeza bwanji kuti mumatikonda?” “Kodi Esau sanali mchimwene wake wa Yakobo?+ Koma ine ndinakonda Yakobo,” watero Yehova. Malaki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:2 Nsanja ya Olonda,5/1/2002, tsa. 1012/1/1987, tsa. 16
2 Yehova wanena kuti: “Ine ndimakukondani anthu inu.”+ Koma inu mwanena kuti: “Mwasonyeza bwanji kuti mumatikonda?” “Kodi Esau sanali mchimwene wake wa Yakobo?+ Koma ine ndinakonda Yakobo,” watero Yehova.