Malaki 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 ‘Mwalinyoza popereka nsembe* zodetsedwa paguwa langa lansembe.’ ‘Inu mukunena kuti: “Takudetsani bwanji?”’ ‘Mwandidetsa ponena kuti: “Tebulo la Yehova+ ndi lonyozeka.” Malaki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:7 Nsanja ya Olonda,12/1/1987, ptsa. 17-18
7 ‘Mwalinyoza popereka nsembe* zodetsedwa paguwa langa lansembe.’ ‘Inu mukunena kuti: “Takudetsani bwanji?”’ ‘Mwandidetsa ponena kuti: “Tebulo la Yehova+ ndi lonyozeka.”