Malaki 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Koma inu mukulinyoza*+ ponena kuti, ‘Palibe vuto kudetsa tebulo la Yehova, ndipo zopereka kapena kuti chakudya chimene chili pamenepo nʼchonyozeka.’+ Malaki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:12 Nsanja ya Olonda,12/1/1987, ptsa. 19-20
12 “Koma inu mukulinyoza*+ ponena kuti, ‘Palibe vuto kudetsa tebulo la Yehova, ndipo zopereka kapena kuti chakudya chimene chili pamenepo nʼchonyozeka.’+