-
Malaki 2:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Mukakana kumvera ndiponso kuganizira nkhani imeneyi mumtima mwanu kuti mulemekeze dzina langa, ndidzakutumizirani temberero+ ndipo madalitso anu ndidzawasandutsa matemberero. Madalitso ndawasandutsa matemberero+ chifukwa nkhani imeneyi simunaiganizire mumtima mwanu,” watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.
-