Malaki 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Tamverani! Chifukwa cha inu, ndiwononga mbewu zanu zomwe mwadzala+ ndipo ndikuwazani ndowe kumaso. Ndikuwazani ndowe za nyama zimene mumapereka nsembe pa zikondwerero zanu. Ndipo mudzanyamulidwa nʼkukaponyedwa pandowezo.* Malaki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:3 Nsanja ya Olonda,12/15/2007, tsa. 265/1/2002, tsa. 15
3 “Tamverani! Chifukwa cha inu, ndiwononga mbewu zanu zomwe mwadzala+ ndipo ndikuwazani ndowe kumaso. Ndikuwazani ndowe za nyama zimene mumapereka nsembe pa zikondwerero zanu. Ndipo mudzanyamulidwa nʼkukaponyedwa pandowezo.*