Malaki 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zikadzatero mudzadziwa kuti ine ndakupatsani lamulo limeneli kuti pangano limene ndinachita ndi Levi lipitirire,”+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.
4 Zikadzatero mudzadziwa kuti ine ndakupatsani lamulo limeneli kuti pangano limene ndinachita ndi Levi lipitirire,”+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.