Malaki 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ankaphunzitsa lamulo la choonadi+ ndipo sanalankhulepo zinthu zoipa. Ankayenda ndi ine mwamtendere komanso mowongoka mtima+ ndipo anabweza anthu ambiri panjira yolakwika. Malaki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:6 Nsanja ya Olonda,5/1/2002, ptsa. 15-16
6 Ankaphunzitsa lamulo la choonadi+ ndipo sanalankhulepo zinthu zoipa. Ankayenda ndi ine mwamtendere komanso mowongoka mtima+ ndipo anabweza anthu ambiri panjira yolakwika.