Malaki 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma inu mwasiya kuyenda panjira yoyenera. Mwachititsa kuti anthu ambiri asiye kutsatira Chilamulo.*+ Ndipo mwaphwanya pangano limene ndinachita ndi Levi,”+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba. Malaki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:8 Nsanja ya Olonda,5/1/2002, tsa. 15
8 Koma inu mwasiya kuyenda panjira yoyenera. Mwachititsa kuti anthu ambiri asiye kutsatira Chilamulo.*+ Ndipo mwaphwanya pangano limene ndinachita ndi Levi,”+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.