Malaki 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Choncho ine ndidzachititsa kuti inu mukhale anthu onyozeka ndi otsika kwa anthu onse, chifukwa simunayende mʼnjira zanga, koma munkakondera pa nkhani zokhudza kutsatira Chilamulo.”+
9 “Choncho ine ndidzachititsa kuti inu mukhale anthu onyozeka ndi otsika kwa anthu onse, chifukwa simunayende mʼnjira zanga, koma munkakondera pa nkhani zokhudza kutsatira Chilamulo.”+