Malaki 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yuda wachita zachinyengo, ndipo mu Isiraeli ndi mu Yerusalemu mwachitika zinthu zonyansa. Chifukwa Yuda wadetsa chiyero* cha Yehova+ chimene Mulungu amachikonda, ndipo Yuda wakwatira mwana wamkazi wa mulungu wachilendo.+ Malaki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:11 Nsanja ya Olonda,5/1/2002, tsa. 177/1/1989, tsa. 316/15/1987, tsa. 11
11 Yuda wachita zachinyengo, ndipo mu Isiraeli ndi mu Yerusalemu mwachitika zinthu zonyansa. Chifukwa Yuda wadetsa chiyero* cha Yehova+ chimene Mulungu amachikonda, ndipo Yuda wakwatira mwana wamkazi wa mulungu wachilendo.+