Malaki 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova adzapha munthu aliyense wochita zimenezi mʼmatenti a Yakobo, kaya akhale ndani.* Adzachita zimenezi ngakhale zitakhala kuti munthuyo amapereka nsembe ngati mphatso kwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.”+ Malaki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:12 Nsanja ya Olonda,5/1/2002, tsa. 17
12 Yehova adzapha munthu aliyense wochita zimenezi mʼmatenti a Yakobo, kaya akhale ndani.* Adzachita zimenezi ngakhale zitakhala kuti munthuyo amapereka nsembe ngati mphatso kwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.”+