-
Malaki 3:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Ndidzakuyandikirani kuti ndikuweruzeni. Sindidzazengereza kupereka umboni wotsutsa amatsenga,+ achigololo, olumbira monama+ komanso amene amachitira zachinyengo munthu waganyu,+ mkazi wamasiye ndi mwana wamasiye*+ komanso amene amakana kuthandiza alendo.+ Anthu amenewa sakundiopa,” watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.
-