Malaki 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Ine sindidzalola kuti dzombe lizidzawononga mbewu zamʼmunda mwanu. Mitengo ya mpesa ya mʼmunda mwanu izidzabereka nthawi zonse,”+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.
11 “Ine sindidzalola kuti dzombe lizidzawononga mbewu zamʼmunda mwanu. Mitengo ya mpesa ya mʼmunda mwanu izidzabereka nthawi zonse,”+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.