Malaki 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Inu mwandinenera mawu achipongwe,” watero Yehova. Ndipo mukunena kuti: “Ife takunenerani zachipongwe zotani?”+
13 “Inu mwandinenera mawu achipongwe,” watero Yehova. Ndipo mukunena kuti: “Ife takunenerani zachipongwe zotani?”+