Malaki 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Panopa tikuona kuti anthu odzikuza akusangalala. Komanso anthu ochita zoipa, zinthu zikuwayendera bwino.+ Iwo amayesa Mulungu koma sakulandira chilango.’”
15 Panopa tikuona kuti anthu odzikuza akusangalala. Komanso anthu ochita zoipa, zinthu zikuwayendera bwino.+ Iwo amayesa Mulungu koma sakulandira chilango.’”