Malaki 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Taonani! Tsiku loyaka ngati ngʼanjo likubwera,+ ndipo anthu onse odzikuza ndi onse ochita zoipa adzakhala ngati mapesi. Pa tsikulo iwo adzawonongedwa moti sipadzatsala mizu kapena nthambi zawo,” watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba. Malaki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:1 Nsanja ya Olonda,12/15/2007, tsa. 295/1/2002, ptsa. 19-214/15/1995, ptsa. 20-228/15/1994, tsa. 3112/1/1992, tsa. 12 Tsiku la Yehova, ptsa. 131-132
4 “Taonani! Tsiku loyaka ngati ngʼanjo likubwera,+ ndipo anthu onse odzikuza ndi onse ochita zoipa adzakhala ngati mapesi. Pa tsikulo iwo adzawonongedwa moti sipadzatsala mizu kapena nthambi zawo,” watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.
4:1 Nsanja ya Olonda,12/15/2007, tsa. 295/1/2002, ptsa. 19-214/15/1995, ptsa. 20-228/15/1994, tsa. 3112/1/1992, tsa. 12 Tsiku la Yehova, ptsa. 131-132