-
Malaki 4:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 “Mudzapondaponda anthu oipa. Iwo adzakhala ngati fumbi kuphazi kwanu pa tsiku limene ndidzachitepo kanthu,” watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.
-