Malaki 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Kumbukirani Chilamulo cha Mose mtumiki wanga. Kumbukirani malamulo ndi ziweruzo zomwe ndinamupatsa ku Horebe kuti Aisiraeli onse azitsatira.+ Malaki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:4 Nsanja ya Olonda,12/15/2007, tsa. 284/15/1995, tsa. 23
4 “Kumbukirani Chilamulo cha Mose mtumiki wanga. Kumbukirani malamulo ndi ziweruzo zomwe ndinamupatsa ku Horebe kuti Aisiraeli onse azitsatira.+