Malaki 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye adzachititsa mitima ya abambo kubwerera kwa ana awo+ ndi mitima ya ana kubwerera kwa abambo awo.* Adzachita zimenezi kuti ine ndisabwere kudzawononga dziko lapansi.” Malaki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:6 Nsanja ya Olonda,9/15/1997, ptsa. 12-154/15/1995, ptsa. 24-259/15/1991, tsa. 22
6 Iye adzachititsa mitima ya abambo kubwerera kwa ana awo+ ndi mitima ya ana kubwerera kwa abambo awo.* Adzachita zimenezi kuti ine ndisabwere kudzawononga dziko lapansi.”