Mateyu 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Jese anabereka Mfumu Davide.+ Davide anabereka Solomo,+ yemwe mayi ake anali mkazi wa Uriya.