-
Mateyu 1:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Choncho mibadwo yonse kuchokera pa Abulahamu kukafika pa Davide inalipo mibadwo 14. Kuchokera pa Davide kukafika nthawi imene Ayuda anatengedwa kupita ku Babulo panali mibadwo 14. Kuchokera pa nthawi imene Ayudawo anatengedwa kupita ku Babulo kukafika pa Khristu, panali mibadwo 14.
-