-
Mateyu 2:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Ndiyeno powatumiza ku Betelehemu, iye anawauza kuti: “Pitani mukamufunefune mwanayo mosamala. Mukakamupeza mubwere kudzandidziwitsa kuti nanenso ndipite kukamugwadira.”
-
-
1. Kuwala Kwenikweni kwa DzikoMalifalensi a Mavidiyo a Uthenga Wabwino wa Yesu
-
-
Okhulupirira nyenyezi anafika komanso Herode anakonza zoti ana aphedwe (gnj 1 50:25–55:52)
-