-
Mateyu 2:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Atalowa mʼnyumbamo, anaona mwana uja ndi mayi ake Mariya ndipo anagwada nʼkumuweramira. Kenako anatulutsa chuma chawo nʼkupereka kwa mwanayo golide, lubani ndi mule monga mphatso.
-
-
1. Kuwala Kwenikweni kwa DzikoMalifalensi a Mavidiyo a Uthenga Wabwino wa Yesu
-
-
Okhulupirira nyenyezi anafika komanso Herode anakonza zoti ana aphedwe (gnj 1 50:25–55:52)
-