-
Mateyu 2:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Choncho Yosefe anadzuka usiku womwewo nʼkutenga mwana uja ndi mayi ake ndipo anachoka kumeneko nʼkupita ku Iguputo.
-
-
1. Kuwala Kwenikweni kwa DzikoMalifalensi a Mavidiyo a Uthenga Wabwino wa Yesu
-
-
Yosefe anatenga Mariya ndi Yesu n’kuthawira ku Iguputo (gnj 1 55:53–57:34)
-