-
Mateyu 2:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Ndiyeno Herode ataona kuti okhulupirira nyenyezi aja amupusitsa, anakwiya koopsa. Choncho anatumiza anthu kukapha ana onse aamuna mʼBetelehemu ndi mʼzigawo zake zonse, kuyambira azaka ziwiri kutsika mʼmunsi. Anasankha kupha ana a zaka zimenezi mogwirizana ndi zimene okhulupirira nyenyezi aja anamuuza.+
-
-
1. Kuwala Kwenikweni kwa DzikoMalifalensi a Mavidiyo a Uthenga Wabwino wa Yesu
-
-
Herode anapha ana onse aamuna ku Betelehemu komanso m’zigawo zake zonse (gnj 1 57:35–59:32)
-