Mateyu 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ine ndikukubatizani mʼmadzi chifukwa chakuti mwalapa,+ koma amene akubwera mʼmbuyo mwanga ndi wamphamvu kuposa ine, ndipo sindili woyenera kumuvula nsapato zake.*+ Ameneyo adzakubatizani ndi mzimu woyera+ komanso moto.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:11 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, article 110 Nsanja ya Olonda,2/15/1992, tsa. 292/1/1992, ptsa. 13-14
11 Ine ndikukubatizani mʼmadzi chifukwa chakuti mwalapa,+ koma amene akubwera mʼmbuyo mwanga ndi wamphamvu kuposa ine, ndipo sindili woyenera kumuvula nsapato zake.*+ Ameneyo adzakubatizani ndi mzimu woyera+ komanso moto.+
3:11 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, article 110 Nsanja ya Olonda,2/15/1992, tsa. 292/1/1992, ptsa. 13-14