Mateyu 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako Yesu anabwera kwa Yohane ku Yorodano kuchokera ku Galileya, kuti iye amubatize.+