Mateyu 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako atachoka ku Nazareti, anafika ku Kaperenao+ nʼkupeza malo okhala mʼmbali mwa nyanja mʼzigawo za Zebuloni ndi Nafitali, Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:13 Yesaya 1, ptsa. 124-126
13 Kenako atachoka ku Nazareti, anafika ku Kaperenao+ nʼkupeza malo okhala mʼmbali mwa nyanja mʼzigawo za Zebuloni ndi Nafitali,