-
Mateyu 4:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 “Anthu amene akukhala mʼdziko la Zebuloni ndi dziko la Nafitali, mʼmbali mwa msewu wakunyanja kutsidya lina la Yorodano, ku Galileya kumene kunkakhala anthu a mitundu ina,
-