Mateyu 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Choncho anthu ambirimbiri ochokera ku Galileya, ku Dekapoli,* ku Yerusalemu, ku Yudeya komanso kutsidya lina la Yorodano, anamutsatira. Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2142
25 Choncho anthu ambirimbiri ochokera ku Galileya, ku Dekapoli,* ku Yerusalemu, ku Yudeya komanso kutsidya lina la Yorodano, anamutsatira.