Mateyu 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Anthu akayatsa nyale saivindikira ndi dengu, koma amaiika pachoikapo nyale ndipo imaunikira onse mʼnyumbamo.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:15 Nsanja ya Olonda,5/15/2008, tsa. 56/1/1997, tsa. 143/15/1987, tsa. 11
15 Anthu akayatsa nyale saivindikira ndi dengu, koma amaiika pachoikapo nyale ndipo imaunikira onse mʼnyumbamo.+