Mateyu 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndithu ndikukuuzani kuti kumwamba ndi dziko lapansi zingachoke mosavuta, kusiyana nʼkuti chilembo chimodzi chachingʼono kwambiri kapena kachigawo kakangʼono ka chilembo cha mʼChilamulo kachoke zinthu zonse zisanachitike.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:18 Nsanja ya Olonda (Yogawira),No. 4 2017, tsa. 13 Nsanja ya Olonda,6/1/1988, tsa. 30
18 Ndithu ndikukuuzani kuti kumwamba ndi dziko lapansi zingachoke mosavuta, kusiyana nʼkuti chilembo chimodzi chachingʼono kwambiri kapena kachigawo kakangʼono ka chilembo cha mʼChilamulo kachoke zinthu zonse zisanachitike.+