-
Mateyu 5:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Choncho aliyense amene waphwanya lililonse la malamulo aangʼono awa nʼkumaphunzitsanso ena kuchita zomwezo, adzakhala wosayenera kulowa mu Ufumu wakumwamba. Koma aliyense wotsatira ndi kuphunzitsa malamulowa adzakhala woyenera kulowa mu Ufumu wakumwamba.
-