-
Mateyu 5:36Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
36 Musamalumbire potchula mutu wanu, chifukwa simungathe kusandutsa tsitsi lanu, ngakhale limodzi, kuti likhale loyera kapena lakuda.
-