Mateyu 5:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Ngati munthu akufuna kukutengera kukhoti kuti akulande malaya ako amkati, uzimupatsanso akunja.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:40 Nsanja ya Olonda,12/15/1998, ptsa. 23-25