-
Mateyu 5:47Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
47 Ngati mukupereka moni kwa abale anu okha, kodi nʼchiyani chachilendo chimene mukuchita? Kodi anthu a mitundu ina nawonso sachita zomwezo?
-