Mateyu 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho mukamapereka mphatso zachifundo,* musamalize lipenga ngati mmene amachitira anthu achinyengo mʼmasunagoge ndi mʼmisewu nʼcholinga choti anthu awatamande. Ndithu ndikukuuzani, anthu amenewo akulandiriratu mphoto yawo yonse. Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:2 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Nsanja ya Olonda,2/15/2009, tsa. 1410/1/1990, ptsa. 15-16
2 Choncho mukamapereka mphatso zachifundo,* musamalize lipenga ngati mmene amachitira anthu achinyengo mʼmasunagoge ndi mʼmisewu nʼcholinga choti anthu awatamande. Ndithu ndikukuuzani, anthu amenewo akulandiriratu mphoto yawo yonse.