Mateyu 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 kuti mphatso zako zachifundo zikhale zachinsinsi. Ukatero Atate wako amene akuona zimene zikuchitika ngakhale kuti iweyo sungathe kuwaona, adzakubwezera.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:4 Nsanja ya Olonda,2/15/2009, tsa. 14 Galamukani!,1/8/1993, tsa. 8
4 kuti mphatso zako zachifundo zikhale zachinsinsi. Ukatero Atate wako amene akuona zimene zikuchitika ngakhale kuti iweyo sungathe kuwaona, adzakubwezera.+